nya-x-nyanja_rev_text_reg/16/02.txt

1 line
170 B
Plaintext

\v 2 Mngelo oyamba anapita na kuthira mbale yake pa ziko; zilonda zoipa ni zobaba zinachoka pa anthu amene anali na chizindikiro cha chilombo, amene anapembeza fano lake.