nya-x-nyanja_rev_text_reg/22/20.txt

1 line
170 B
Plaintext

\v 20 wamene acitira umboni ku zinthu izi anene, "inde! ndibwera manje-manje." amen! bwerani , ambuye yesu! \v 21 chisomo cha ambuye yesu chikhale na wina aliyense. amen.