nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/17.txt

1 line
346 B
Plaintext

\v 17 Mngelo wina anatuluka ku mwamba mu nyumba ya Mulungu; nayeve anali na chikwakwa. \v 18 Mngelo winanso anatuluka kuchoka pa guwa la zonunkhirisa, amene anali na ulamuliro pa muliro. Anaitana na mphamvu uja amene anali na chikwakwa chonola, "Tenga chikwakwa chako na kuika pamozi zidunswa za mpesa m'minda ya ziko, chifukwa mpesa wake wapya."