nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/14.txt

1 line
500 B
Plaintext

\v 14 Ninayangana, ndipo panali makumbi yoyera. Ndipo onkhala pa makumbi anali ngati mwana wa munthu. Anali na kolona ya golide pa mutu pake na chikwakwa chonola ku manja yake. \v 15 Ndipo mngelo wina anatuluka mu nyumba ya Mulungu ndipo anaitana na mau okweza kuitana uja amene ali pa makumbi: "Tenga chikwakwa chako elo uyambe kujuba. Chifukwa nthawi yojuba yakwana, cifukwa zokolola pa ziko zapya." \v 16 Ndipo wamene anali pa makumbi anayamba kuyendesa chikwakwa pa ziko, ndipo ziko inakololedwa.