nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/11.txt

1 line
305 B
Plaintext

\v 11 Utsi wa kunzunzika kwao upitilira ku mwamba nthawi zonse, ndipo sapumula usana na usiku-awa opembeza chilombo na fano lake, na aliyese amene analandira chizindikiro cha zina lake. \v 12 Apa pali kufunika kupilira kwa iwo amene ni oyera, amene akonkha malamulo ya Mulungu na chikhulupiliro mwa Yesu."