nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/08.txt

1 line
168 B
Plaintext

\v 8 Mngelo wina-mngelo wachiwiri- anasatira kukamba kuti, "Wagwa, wagwa Babylon wamphamvu, wamene anauza anthu onse kuti amwe vinyo wa zilakolako zake za chiwelewele."