nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/06.txt

1 line
362 B
Plaintext

\v 6 Ninaona mngelo wina akuuluka mu mwamba, amene anali na uthenga wa moyo ouza anthu onkhala pa ziko la pansi-ku maiko onse, mitundu yonse, chilankhulo na anthu. \v 7 Anaitana na mau a mphamvu, "yopani Mulungu na kumupasa ulemelero. Chifukwa nthawi ya chiweruzo chake chafika. Mulambileni, wamene anapanga kumwamba, dziko la pansi, nyanja, na nyenje za manzi."