nya-x-nyanja_rev_text_reg/14/01.txt

1 line
306 B
Plaintext

\c 14 \v 1 Ninaona na kuona mwana wa nkhosa oimilira pa phiri la Zion. Anali na anthu 144,000 amene anali na zina lake na zina la Atate ake yolembewa pa mphumi zao. \v 2 Ninamvera mau ochokera kumwamba omveka monga manzi yambiri na kugunda kwa mphamvu. Mau omwe ninamvera yanali monga anthu oliza mitoliro.