nya-x-nyanja_rev_text_reg/03/14.txt

1 line
362 B
Plaintext

\v 14 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodicea lemba: Aya ni mau ya ma Amen, mboni ya zoona na yodalilika, olamulira chilengedwe cha Mulung u. \v 15 Niziba zamene mwachita, kuti sindinu otentha kapena ozizira. Chinakankhala bwino kuti munali otentha kapena ozizira! Tsono, \v 16 chifukwa muli pakati-kati- simuli otentha kapena ozizira- nizakulabvulani mkamwa mwanga.