\v 10 Nina tenga kabuku kakang'ono kucoka ku manja a mngelo na kudya. Inali yonzuna monga uci mukamwa mwanga, nitasiliza kudya, mumala mwanga munababa. \v 11 Pamene apo wina anakamba na ine, ukambenso za anthu ambili, mitundu, malilime na mamfumu."