\v 5 \v 6 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha chitatu, ninamvera chamoyo cha chitatu kukamba ati, "bwera!" ninaona kavalo wakuda, ndipo wamene anakwerapo ananyamula muyeso m'manja mwake. Ninamvera mau yamene yanamveka kwati niya chimozi mwa zamoyo kukamba ati, "muyeso wa tiligu oguliwa dinari imodzi, ndi miyeso itatu ya balele yogulidwa dinari imozi. Koma osaononga mafuta na vinyo."