\v 5 Pambuyo pa izi zinthu ninaona, ndipo tenti ya mboni inaseguliwa ku mwamba. \v 6 Kuchoka pa malo oyera panachoka angelo 7 onyamula zilango 7. Anavala zobvala zoyera, zonyezimila ndi sashi ya golide yozungulira chifuwa chao.