\v 8 Mngelo wa chiwiri analiza lipenga lake, ndipo chinthu china chachikulu monga phiri chinaponyedwa mnyanja. Gawo lina la manzi inankhala magazi, \v 9 zina mwa nyama za m'manzi zinafa, ndipo ma bwato ambiri anaonongeka.