\c 8 \v 1 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 7, kunali chete ku mwamba kwa theka la ola limozi. \v 2 Ndipo ninaona angelo 7 amene ankhala pa mpando wa chimfumu wa Mulungu, ndipo malipenga 7 yanapasidwa kwa iwo.