\v 6 Ninaona mwana wa nkhosa kuimilira pakati pa mpando wa chimfumu na zamoyo zinai ndinso pakati pa akulu 24. Anaoneka monga anali ataphedwa. Anali na manyanga 7 na menso 7; Aya ni mizimu 7 ya Mulungu yotumizidwa ku dziko lonse lapansi. \v 7 Anapita ndi kukatenga buku lija ku dzanja la manja la yemwe akhala pa mpando wa chimfumu.