\v 16 mzinda unali olingana mbali zonse; utali wake unali olingana na ukula kwake. anapima mzinda na kopimila, 12000 kutalika kwake (kutalika, m'mimba ni kukula kwake kunali chimozi-mozi). \v 17 anapimaso mpanda wake 144 cubits unenepa kwake kulingana na kupima kwa munthu (komwe ni kupimanso kwa mngelo).