\v 5 Sibanapasidwe mphamvu zakupha anthu, koma kuwavutisa chabe kwa miyezi isanu. Ululu wake unali monga wa kaliza ngati waluma munthu. \v 6 Masiku ameneo anthu azafuna imfa, koma osaipeza. Azafuna maningi kuti afe, koma imfa izathaba.