\v 7 tiyeni tikondwere na kunkhala okondwa na kumupasa ulemu chifukwa chisangalalo cha ukwati wa mwana wa nkhosa chafika, elo mkazi wa chikwati wakonzeka. \v 8 Analoledwa kuti abvale zovala zowala na zopanda dothi" (chifukwa zovala zopanda dothi ni zincito za anthu oyera).