\v 17 muzimu na mkazi okwatiriwa unena, "bwera! "lekani wamene amvera anene, "bwerani!" iye wamene ali na njota, lekani abwere, na wamene acifunisisa, lekani alandire manzi ya moyo mwa ulele.