\v 6 Ninaona kuti mkazi anali wokolewa na magazi ya bokhulupilila na magazi ya bopaiwa pa cifukwa ca Yesu. Pamene nina muona, nina dabwisiwa kwambili. \v 7 Koma mngelo ananena kuli ine, "wadabwila ciani? nizakufotokozerani tanthauzo ya mkazi na cinyama camene cimunyamula, cilombo camene cili na mitu 7 na nyanga 10