\v 15 Ndipo mungelo wa chisano na vibili analiza lipenga, ndipo ma liu yakulu yanakamba kumwamba, "Umfumu wapa ziko ya pansi wankala ufumu wa Mbuye watu na Kristu wake. Azalamulila muyayaya.