\v 7 12,000 kuchoka ku mtundu wa Simeon, 12,000 kuchoka ku mtundu wa L evi, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Isaacher, \v 8 12,000 kuchoka ku mtundu wa Zebulun, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Yosefe ndipo 12,000 kuchoka ku mtundu wa Benjamin analandira zizindikiro.