Thu Dec 26 2019 18:59:52 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Muzgatama 2019-12-26 18:59:53 +02:00
commit ec64f8afa6
84 changed files with 94 additions and 4 deletions

1
01/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 1 \v 1 \v 2 \v 3 Ili ni vumbuluso la Yesu Kristu lamene Mulungu anamupasa kuti aonese akapolo ake zamene zizacitika manje-manje. Anazionesa kupitira mwa mngelo wake kwa Yohane. Yohane anacitira umboni mau a Mulungu na pa umboni operekedwa wa Yesu Khristu, zinthu zonse zamene anaona. Ni odala amene abelenga mokweza, na amene amvera mau ya uneneri, na bamene bagonjera zamene zinalembedwamo, cifukwa nthawi ili pafupi.

1
01/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 \v 5 \v 6 Yohane, ku mipingo isanu na iwiri ya ku Asiya: Cisomo ni mtendere kucokera kwa iye amene analiko, aliko ndipo azankhalako, ni kwa mizimu isanu ni iwiri yamene yankhala pa mpando wa cimfumu, na kwa Yesu Khristu, amene ni mboni yokhulupirika, mwana oyamba kucoka pa akufa, ni olamulira mamfumu a dziko lapansi. Kwa iye wamene atikonda ndipo anatiombola ku machimo athu ni magazi yace- watipanga kunkhala umfumu, ansembe a Mulungu wake Atate- kwa iye kunkhale ulemelero ni mphamvu kwa nthawi zonse. Amen.

1
01/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 \v 8 Onani, azabwera mu makumbi; ndipo diso lililose lizamuona, kuikapo naonse bamene banamulasa. Ziko lonse lizalira chifukwa cha yeve. Inde, Amen. "Ndine oyamba na osiliza," akamba ambuye Mulungu, "amene analiko, aliko, elo azankhalako, wa mpamvu zonse."

1
01/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Ine, Yohane-m'bale wanu amene agabana na inu zobvuta na kupilira zamene zipezeka mwa Yesu- ninali pa malo ozungulilidwa na manzi ya Patmos kamba ka mau ya Mulungu na umboni wa Yesu. Ninali mu mzimu wa siku la ambuye. Ninamvera kumbuyo kwanga mau okuwa omveka monga lipenga. Yanakamba ati, "lemba zamene uona mu buku, elo uzitume ku mipingo isanu na iwiri- ku Efeso, ku Smyrna, ku Pergamum, ku Thyatira, ku Sardis, ku Philadelphia na ku Laodicea."

1
01/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 \v 13 Ninapindamuka kuti nione ni mau ya bandani yamene yenze kunikambisa, pamene ninapindamuka ninaona pofaka nyale pagolide pali 7. Pakati pa nyale panali wina wamene anaoneka monga mwana wa munthu, anabvala mukanjo utali maningi wamene unafika ku mendo yake na sashi ya golide kuzungulira chifuba chake.

1
01/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 \v 15 \v 16 Mutu wake na sisi zinali zoyera monga thonje- zoyera monga matalala, elo menso yake yenze yosweta monga muliro. Mapazi yake yenze yobeka monga ni bronze, bronze yakuti baifaka pa muliro, elo mau yake yenzomveka monga ni manzi yambiri. Enze anagwira nyenyezi 7 kumanja yake, na mpeni wamene uchekera mbali zonse unali kuchoka mukamwa mwake. Pamenso pake penzowala monga ni zuba.

1
01/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 \v 18 Pamene ninamuona, ninagwa pansi pa mendo yake monga munthu wakufa. Anafaka zanja yake pali ine ndipo anakamba ati, "usayope. ndine oyamba na osiliza, na wamene ankhala na moyo. Ninali wakufa, koma onani, ninkhala wa muyayaya! elo nili na mfungulo ya imfa na hade.

1
01/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 \v 20 Manje, lemba zamene waona, zamene zilipo manje, na zamene zizachitika kusogolo. Koma pa tanthauzo lobisika la nyenyezi zamene waona mumanja mwanga, na poika nyale pa golide pali 7: Nyenyezi 7 ni angelo 7 a mipingo 7, ndipo poika nyale pali 7 ni mipingo.

View File

@ -1 +1,5 @@
Ici nichivumbuluso cha yesu kristu ana mupasa kulangiza apuzisi ake ndipo chizachitika manje manje .
<<<<<<< HEAD
Ici nichivumbuluso cha yesu kristu ana mupasa kulangiza apuzisi ake ndipo chizachitika manje manje .
=======
Mutu 1
>>>>>>> e420be4f253cdc4b36bad4180b49a52aeb350723

1
02/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 2 \v 1 \v 2 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Efeso lemba: aya ndiye mau ya amene anyamula nyale 7 ku zanja la manja na amene ayenda pakati pa zoikapo nyale 7 za golide, "niziba zamene wachita na nchito zanu za mphamvu na kupilira mtima kwanu. Niziba ati simunyengelera banthu oipa. Niziba ati munayesa onse amene amaziyesa a positoli, koma si apositoli, elo mwabapeza kuti ni ba boza.

1
02/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Niziba kuti ndinu banthu olimbikira, elo mwabvutika maningi chifukwa cha zina langa, ndipo simunaleme. Koma nili chabe na bvuto imozi pali imwe yakuti mwasiya chikondi chamene munali nacho poyamba. Kumbukirani sono kwamene mwagwera. Siyani zoipa na kuchita zamene munali kuchita poyamba. Ngati simuleka zoipa, nizabwera kuchosapo poika nyale kuchoka pa malo pamene ilili.

1
02/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 \v 7 Koma muli na ichi: simukonda zamene ma Nicolaitans bachita, zamene naine nizonda. Lekani wamene ali na matu yakumva amvere zamene mzimu akamba kwa mipingo. Kwa amene apambana, nizamupasa mwai wakudya mu mtengo wa moyo, wamene uli mu paradiso ya Mulungu.

1
02/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 \v 9 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Smyrna lemba: Aya ni mau ya yeve wamene ni oyamba na osiliza, yeve wamene enze anafa nouka futi: niziba kubvutika kwanu na kusauka kwanu, koma ndimwe olemera. Niziba manyozo ya bamene bakamba ati ni ba yuda, koma si bayuda. Nimipingo ya satana.

1
02/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 \v 11 Musayope zoipa zamene muzapitamo. Onani! satana azaponya benangu ba inu mu ndende kuti mukayesedwe, ndipo muzabvutika kwa masiku 10. Nkhalani okhulupirika mpaka kufa, elo nizakupasani kolona ya moyo. Lekani amene ali na matu ya kumva amvere zamene mzimu ukamba kwa mipingo. Iye amene apambana sazaonongeka na imfa ya chiwiri.

1
02/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 \v 13 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Pergamum lemba: Aya ni mau ya wamene ali na mpeni wonola konse-konse. Niziba kwamene munkhala, uko kwamene mpando wa satana upezeka. Koma mupitilira kugwira zina langa. Niziba kuti simunakane chikhulupiliro chanu muli ine, angankhale mu nthawi ya Antipas, mboni yanga, okhulupilika wanga, amene anapaiwa pakati panu, uko kwamene satana ankhala.

1
02/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 \v 15 Koma nili na tunthu tung'ono pali imwe: Muli na banthu benangu bamene bagwilirira maningi pa chipunziso cha Balaam, wamene anapunzisa Balak kuika zinthu zoipa pali bana ba Israel, kuti badye chakudya cha vibanda na kunkhala banthu ba chiwelewele. Chimozi-mozi, muli na benangu bamene banasunga chipunziso cha Nicolaitans.

1
02/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 \v 17 Siyani zoipa sopano! ngati simuzaleka, nizabwera kwa inu mwamsanga, elo nizachita nkhondo na beve na lupanga ili mu kamwa mwanga. Lekani wamene ali na matu amvere zamene mzimu ukamba ku mipingo. Iye amene apambana, nizamupasa manna yamene yanabisiwa, elo nizamupasa mwala oyera wamene panalembedwa dzina lasopano, dzina lamene palibe winangu amene aziba koma wamene apasidwa chabe.

1
02/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 \v 19 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Thyatira lemba: Aya ni mau ya mwana wa Mulungu, amene ali na menso monga moto na mapazi monga bronze yowala: "Niziba zamene mwachita: chikondi chanu na chikhulupiliro na zinchito na kulimbikira kwanu. Niziba kuti zamene muchita manje zichira zamene munachita kudala.

1
02/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 \v 21 Koma nili na kanthu aka pa inu: Mumamulekelera mkazi Yezebeli, amene amazikamba ati ni muneneri. chifukwa cha zopunzisa zake asokoneza bambiri bakapolo banga kuti bazichita chiwelewele, nakudya chakudya chamene chapasidwa kwa vibanda. Nimamupasa nthawi kuti aleke zoipa, koma safuna kuleka chiwelewele chake.

1
02/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 \v 23 Onani! nizamuponyera pa bedi ya odwala, na onse amene achita naye chigololo bazabvutika maningi, malinga ngati sibaleka zoipa zake. Nizamupaila bana bake, elo mipingo yonse yazaziba ati ndine amene nimaona maganizo na mitima ya banthu. Nizapasa aliyense wa inu kulingana na zamene muchita.

1
02/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 \v 25 Koma kwa inu benangu baku Thyatira, aliyense amene sazasunga chipunziso ichi, ndipo sibaziba zinthu zobisika zapansi za satana- kwa inu nikamba, 'ine sinizakupasani zinango zolemesa.' Mu njira iliyonse, mufunika kunkhala olimba mpaka nikabwere.

1
02/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 \v 27 \v 28 \v 29 Wamene apambana nakuchita zamene nachita mpaka pothera, kwa yeve nizapasa ulamuliro pa maiko onse. Azalamulira maiko na mphamvu, azabapwanya monga mbiya ya dothi. Monga mwamene nalandilira kuli atate, nizamupasaso naine nyenyezi ya m'mawa. Lekani wamene ali na matu amvere zamene mzimu ukamba kwa mipingo.

1
02/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 2

1
03/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 3 \v 1 \v 2 "Kwa mngelo wa ku Sardis lemba: Aya ni mau ya wamene asunga mizimu 7 ya Mulungu na nyenyezi 7." Niziba zamene mwachita. Muli na mbiri yakuti muli na moyo, koma ndinu bakufa. Ukani na kulimbisa zamene zankhalako, koma zifuna kufa, chifukwa sininapezeko nchito iliyonse yabwino pamaso pa Mulungu wanga.

1
03/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 Kumbukirani, sopano, zamene munalandira na kumvera. Gonjerani, na kulapa. Koma ngati simuzauka, nizabwera monga kawalala, elo simuzaziba nthawi yamene nizabwelera kwa inu. Koma pali maina yang'ono chabe ya banthu mu Sardis bamene sibanafipise vovala vao. Bazayenda naine, mu zobvala zoyera, chifukwa nioyenera.

1
03/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 \v 6 Wamene apambana azapasiwa zobvala zoyera, elo sinizachosa dzina lake mu buku la moyo, ndipo nizakamba za dzina lake kwa atate, na angelo ao. Lekani amene ali na matu amvere zamene mzimu akamba ku mipingo.

1
03/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Onani! onse amene achokera ku mpingo wa satana, iwo amene akamba ati ni bayuda koma sibayuda; anama chabe boza. Nizabapanga kuti babwere bagwade pa mapazi yanu, ndipo bazaziba kuti nikukondani. Chifukwa mwasunga malamulo anga mopilira, naine nizakusungani pa nthawi ya mayeso yamene ibwera padziko lapansi, kuyesa onse amene ankhala pa dziko. Nibwera manje-manje. Sungani bwino zamene muli nazo kuti anthu asalande kolona yanu.

1
03/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 \v 13 Nizapanga amene alimbikira kunkhala nsandamila ya mnyumba ya Mulungu, ndipo sazatulukamo. Nizalemba dzina la Mulungu pa iye, dzina la mzinda wa Mulungu wanga (Yerusalemu wasopano, wamene uchoka kumwamba kwa Mulungu wanga), na dzina langa lasopano. Lekani wamene ali na matu amvere zamene mzimu ukamba ku mipingo.

1
03/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 \v 15 \v 16 Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodicea lemba: Aya ni mau ya ma Amen, mboni ya zoona na yodalilika, olamulira chilengedwe cha Mulung u. Niziba zamene mwachita, kuti sindinu otentha kapena ozizira. Chinakankhala bwino kuti munali otentha kapena ozizira! Tsono, chifukwa muli pakati-kati- simuli otentha kapena ozizira- nizakulabvulani mkamwa mwanga.

1
03/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 \v 18 Mukamba kuti, ndinu olemera, nili na zinthu zambiri, ndipo sinifuna kalikonse. Koma simuziba kuti ndinu ochitisa chifundo maningi, osauka, osapenya ni osabvala. Mvelani zamene nikamba: Gulani kwa ine golide oikidwa mu moto kuti munkhale olemera na zobvala zoyera zowala kuti mubvale musaonese manyazi ya umaliseche wanu, na mankhwala ya m'maso kuti uone bwino.

1
03/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 \v 20 Nimazuzula aliyense wamene nikonda, ni kuwauza mwamene ayenera kunkhalira. Kotero, cita changu na kutembenuka. Onani! naima pa khomo nigogoda. Ngati wina amvera mau anga na kusegulako, nizaloba mnyumba yake nakudya nayeve, yeve na ine.

1
03/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 \v 22 Wamene apambana, nizamupasa mwai onkhala na ine pa mpando wa chimfumu, mwamene ine ninapambana na kunkhala na atate pa mpando wa chimfumu. Lekani wamene ali na matu amvere zamene mzimu ukamba kwa mipingo.

1
03/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 3

1
04/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 4 \v 1 \v 2 \v 3 Pambuyo pa izi zinthu ninayang'ana, ndipo ninaona chiseko choseguka kumwamba. Mau oyamba omwe ninamva omwe yamakamba na ine monga lipenga kukamba ati, "bwera kuno, ndipo nizakuuza zamene zizachitika pambuyo pa izi." Pa nthawi imeneyi ninali mu mzimu, ndipo ninaona kunali mpando wa chimfumu ku mwamba, ndipo panali wina onkhalapo. Wamene analipo amaoneka monga jasper na carnelian. Panali utawaleza kuzungulira pa mpando wa mfumu. Utawaleza unaoneka umaoneka monga mwala wa emerald.

1
04/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 \v 5 Kuzugulira mpando panaliso mipando 24, ndipo amene anankhala pa mipando imeneyi ni banthu bakulu-bakulu, obvala zobavala zoyera, na ma kolona ya golide ku mutu yao. Pa mpando wa chimfumu panachoka moto wa kaleza, kugunda na kung'anima kwa mphenzi. Nyale 7 zimayaka pasogolo pa mpando, nyale zomwe ni mizimu 7 ya Mulungu.

1
04/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Pasogolo pa mpando panali msinje wa galasi, monga kirisito. Pakati pa mpando ndi kuzungulira panali zamoyo zinai, zamenso yambiri, kusogolo na kumbuyo.

1
04/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 \v 8 Chamoyo choyamba chenze kuoneka monga nkhalamu, cha chiwiri chenze kuoneka monga mwana wa ng'ombe, cha chitatu monga pa menso pa munthu, ndipo cha namba 4 chinali kuoneka monga mbalani youluka. Zamoyo zimenez chilichonse chinali na mapiko 6, yozula menso pansi na pamwamba. Usiku na muzuba sivileka kukamba ati, "Oyera, Oyera, Oyera ni Mulungu wa mphamvu zonse amene analiko, aliko, ndipo azankhalako."

1
04/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Nthawi zonse pamene za moyo zipereka ulemelero, ulemu na matamando kwa amene ankhala pa mpando wa chimfumu, wamene ankhala kwa muyaya, akulu 24 amazigwesa pansi kulambira iye amene ankhala pa mpando wa chimfumu. Bamagwada kwa iye amene ankhala muyaya, ndipo amaponya pansi ma kolona yao ku mpando, kukamba kuti, "Ndinu oyenera, ambuye athu na Mulungu wathu, kulandira ulemu, ulemelero ndi mphamvu. Chifukwa munalenga zinthu zonse, ndipo mwa chifuniro chanu, zinankhalako ndipo zinalengewa."

1
04/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 4

1
05/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 5 \v 1 \v 2 Ndipo ninaona mumanja mwa iye amene anakhala pa mpando wa chimfumu ku dzanja la manja lake, chi buku cholembewa mbali zonse ziwiri. Inali yosindikiziwa na zosindikizira 7. Ninaona mngelo wa mphamvu kukuwa ni mau okweza, "Ndani oyenera kusegula buku na zosindikizira zake?"

1
05/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Palibe aliyense kumwamba, padziko la pansi kapena pansi pa dziko yemwe anali oyenera kusegula buku kapena kuwerenga. Ninalira maningi chifukwa panalibe aliyense oyenera kusegula kapena kuwerenga buku. Koma m'mozi wa akulu-akulu anati kwa ine, "Usalire. Ona! nkhalamu ya mtundu wa ayuda, muzu wa Davide, wapambana. Akwanisa kusegula buku na kusegula zosindikizira zake."

1
05/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 \v 7 Ninaona mwana wa nkhosa kuimilira pakati pa mpando wa chimfumu na zamoyo zinai ndinso pakati pa akulu 24. Anaoneka monga anali ataphedwa. Anali na manyanga 7 na menso 7; Aya ni mizimu 7 ya Mulungu yotumizidwa ku dziko lonse lapansi. Anapita ndi kukatenga buku lija ku dzanja la manja la yemwe akhala pa mpando wa chimfumu.

1
05/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Pamene mwana wa nkhosa anatenga buku, za moyo zinai ndi akulu 24 anagwa pansi kumulambira. Aliyense anali na mtolilo na mbale yodzala ndi zinthu zonunkhira, yomwe ni ma pemphero ya okhulupilira.

1
05/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 \v 10 Anaimba nyimbo ya sopano: Ndinu oyenera kutenga buku ndi kulisegula zosindikizira zake. Chifukwa munaphedwa, ndipo na magazi anu munagula anthu a mitundu yonse kwa atate, chilankhulo, mtundu, anthu na maiko. Munawapanga ufumu, ndi ansembe kutumikira Mulungu wathu, ndipo azakhala pa dziko la pansi."

1
05/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 \v 12 Ndipo ninaona ndi kumva mau ya angelo ambiri kuzungulira mpando wa chimfumu, zamoyo zinai ndi akulu 24. Unyinji wao unali zikwi ndi zikwi. Ananena mu mau okweza, "Ndi oyenera mwana wa nkhosa yemwe anaphedwa kulandira mphamvu, ulemelero,nzeru, ulemu na matamando."

1
05/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 \v 14 Ninamva cholengedwa chilichonse kumwamba, padziko la pansi, na pansi pa dziko la pansi ni mu manzi- zonse zopezekamo- kukamba ati, "kwa iye okhala pa mpando wa chimfumu na kwa mwana wa nkhosa, kukhale matamando, ulemu, ulemelero ndi mphamvu zolamulira nthawi zonse." Zamoyo zinai zinati, "Amen!" ndipo akulu anazigwesa pansi ndi kulambira.

1
05/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 5

1
06/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 6 \v 1 \v 2 Ninaona pamene mwana wa nkhosa anasegula imozi mwa zosindikizira 7, ndipo ninamva cimozi mwa zamoyo zinai zija kukamba kuti mu mau amene anamveka monga mabingu, "Bwera!" Ninaona ndipo panali kavalo oyera. Okwerapo ananyamula uta, ndipo anapasiwa kolona. Anachoka ngati opambana kuti apambane.

1
06/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha chiwiri, ninamvera chamoyo chachiwiri kukamba ati, "bwera!" Ndipo kavalo anatuluka osweta. Wamene anakwerapo anapasidwa mphamvu yochosa mtendere pa dziko la pansi, kuti anthu aphane okha-okha. Okwerapo ameneyu anapasidwa chimpeni chachikulu.

1
06/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 \v 6 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha chitatu, ninamvera chamoyo cha chitatu kukamba ati, "bwera!" ninaona kavalo wakuda, ndipo wamene anakwerapo ananyamula muyeso m'manja mwake. Ninamvera mau yamene yanamveka kwati niya chimozi mwa zamoyo kukamba ati, "muyeso wa tiligu oguliwa dinari imodzi, ndi miyeso itatu ya balele yogulidwa dinari imozi. Koma osaononga mafuta na vinyo."

1
06/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 \v 8 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 4, ninamvera mau ya chamoyo cha chinai kukamba ati, "bwera!" ndipo ninaona kavalo ombuwilira. Ndipo okwerapo dzina lake ni imfa, ndipo hade anali kulondola kumbuyo. Anapasidwa mphamvu ya gawo la dziko, kupha na chimpeni, njala na matenda na nyama za musanga za padziko.

1
06/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chosindikizira cha namba 5, ninaona pansi pa guwa mizimu ya aja omwe anaphedwa chifukwa cha mau a Mulungu na umboni omwe anali nao. Analira na mau okweza, "Mpaka liti, olamulira onse, oyera ndi wachoonadi, pomwe muzaweruza omwe ankhala pa dziko la pansi, pomwe muzabwezera magazi athu?" Ndipo aliyense wa iwo anapasidwa mkanjo oyera, ndipo anauzidwa kuti ayembekeze pang'ono mpaka nambala ya akapolo anzao na bale ao ikwane omwe ayenera kuphedwa, monga momwe iwo anaphedwa.

1
06/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 \v 13 \v 14 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 6, ninaona ndipo panali chibvomezi champhamvu. Dzuwa inada monga chovala chakutha ndipo mwezi unakhala monga magazi. Nyenyezi za kumwamba zinagwa pansi, monga mwamene mtengo wa mkuyu umagwesera zipaso zake zosapya ngati mphepo yakuntha. Kumwamba kunasoba monga buku lamene alupeteka. Mapiri na zitunda zinachosedwa pa malo ake.

1
06/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 \v 16 \v 17 Ndipo mamfumu na anthu olemekezeka, akulu a asilikali, olemera, amphamvu, ena onse, omasuka ni akapolo, anabisala mu mphanga na mu minyala ya m'mapiri. Ananena kwa miyala na mapiri, "Tigweleni!" tibiseni ku nkhope ya iye amene ali pa mpando wa chimfumu ni ku mkwiyo wa mwana wa nkhosa. Chifukwa siku la mphamvu la mkwiyo wao lafika. Ndani azakwanisa kuimilira?"

1
06/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 6

1
07/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 7 \v 1 \v 2 \v 3 Pambuyo pa izi ninaona angelo anai oimilira pa makona anai a dziko, kubweza mwa mphamvu mphepo zinai za dziko kuti mphepo iliyonse isathire pa dziko la pansi, pa nyanja, kapena pa mtengo ulionse. Ni naona mngelo wina kuchokera ku m'mawa, amene anali na chizindikiro cha Mulungu wa moyo. Analira mokweza kwa angelo anai aja omwe anapasidwa mphamvu yoononga dziko la pansi na nyanja: "Osaononga dziko la pansi, nyanja ndi mitengo mpaka pamene tizaika zizindikiro pa mphumi pa akapolo a Mulungu."

1
07/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 \v 5 \v 6 Ninamva nambala ya anthu amene anaikidwa zizindikiro: 144,000, omwe anaikidwa chizindikiro kuchoka ku mtundu ulionse wa anthu a Israel: 12,000 ochokera mju mtundu wa yuda anaikidwa zizindikiro, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Reuben, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Gad, 12,000 kuchoka ku mtundu Asher, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Naphtaly, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Manasseh.

1
07/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 \v 8 12,000 kuchoka ku mtundu wa Simeon, 12,000 kuchoka ku mtundu wa L evi, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Isaacher, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Zebulun, 12,000 kuchoka ku mtundu wa Yosefe ndipo 12,000 kuchoka ku mtundu wa Benjamin analandira zizindikiro.

1
07/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 \v 10 Pambuyo pa zinthu izi ninaona, ndipo panali anthu ambiri amene palibe angawerenge-kuchoka ku maiko onse, mtundu, anthu na chilankhulo-kuimilira pa mpando wa chimfumu ni mwana wa nkhosa. Anali atamvala zobvala zoyera, ndipo ananyamula nthambi za kanjeza m'manja mwao, ndipo anali kukamba na mau okweza: " Chipulumuso chichokera kwa Mulungu wathu amene ankhala pa mpando wa chimfumu ni kwa mwana wa nkhosa!"

1
07/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 \v 12 Angelo onse anali oimilira kuzungulira mpando wa chimfumu na kuzungulira akulu komanso zamoyo zinai, ndipo anagwa pansi kuyang'ana nkhope zao pansi kulambira pa mpando wa chimfumu. Anapembeza Mulungu, kukamba kuti, "Amen! matamando, ulemelero, nzeru, mayamiko, ulemu, mphamvu, zinkhale kwa Mulungu nthawi zonse! Amen!"

1
07/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 \v 14 M'modzi wa akulu ananifunsa ine kuti, "ndani awa, omwe abvala mikanjo yoyera, ndipo achokera kuti?" Ninakamba nayeve kuti, "bwana, mudziwa" ndipo anati kwa ine, "Awa ndi anthu amene anachoka mu manzunzo yowawa. Awasha mikanjo yao na kuyayeretsa na magazi ya mwana wa nkhosa.

1
07/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 \v 16 \v 17 Pa chifukwa ichi, ali pa maso pa mpando wa Mulungu, ndipo amiupembeza usana na usiku mu nyumba yake. Iye wamene ankhalaa pa mpando wa chimfumu azaika tenti yake pa iwo. Sazamveranso njala, kapena kumvera ludzu. Dzuwa sizawagwesa, kapena kutenthewa. Chifukwa mwana wa nkhosa pakati pa mpando azankhala mbusa wao, ndipo azawapereka ku malo a manzi ya moyo, ndipo Mulungu azapukuta misozi mu menso yao."

1
07/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 7

1
08/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 8 \v 1 \v 2 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 7, kunali chete ku mwamba kwa theka la ola limozi. Ndipo ninaona angelo 7 amene ankhala pa mpando wa chimfumu wa Mulungu, ndipo malipenga 7 yanapasidwa kwa iwo.

1
08/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Mngelo wina anabwera, ananyamula mbale ya golide ya zonunkhirisa, kuimilira pa guwa la zonunkhirisa. Zonunkhirisa zambiri zinapasidwa kwa iye kuti apereke pamozi na mapemphero ya okhulupilira pa guwa la zonunkhirisa pa mpando wa chimfumu. Utsi wa zonunkhirisa, na mapemphero ya okhulupirira, yanafikira ku mpando wa Mulungu kuchoka ku manja ya mngelo. Mngelo anatenga mbale ya zonunkhira na kuikamo moto wa pa guwa. Ndipo anaiponya pansi pa dziko la pansi, ndipo panali phokoso la kaleza, kugunda na kung'anipa kwa mphenzi, na chibvomezi.

1
08/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 \v 7 Angelo 7 omwe anali na malipenga anakonzeka kuti alize. Mngelo oyamba analiza lipenga lake, ndipo panali mvula ya mphepo, moto yosakaniza na magazi. Inaponyedwa pa dziko la pansi kwakuti gawo lina linatenthedwa, gawo la mitengo inapya, ndi udzu onse obiliwira unapya.

1
08/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 \v 9 Mngelo wa chiwiri analiza lipenga lake, ndipo chinthu china chachikulu monga phiri chinaponyedwa mnyanja. Gawo lina la manzi inankhala magazi, zina mwa nyama za m'manzi zinafa, ndipo ma bwato ambiri anaonongeka.

1
08/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 \v 11 Mngelo wachitatu analiza lipenga lake, ndipo nyenyezi yaikulu inagwa kuchoka ku mwamba, yoyaka monga tochi, pa gawo lalikulu la misinje na nyenje za madzi. Dzina la nyenyezi ni chobaba. Ndipo madzi yanankhala yobaba, ndipo anthu ambiri anafa chifukwa cha manzi yobaba.

1
08/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Mngelo wa chinai analiza lipenga lake, ndipo gawo lina la dzuwa linakanthiwa, ndi gawo lina la mwezi na gawo lina la nyenyezi. Sono magawo ambiri anadesedwa; gawo lina la siku na gawo lina la usiku linalibe kuwala.

1
08/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Ninaona, ndipo ninamva mphungu yomwe imauluka pakati pa mitambo, kuitana na mau yokweza, "tsoka, tsoka, tsoka, kwa amene ankhala pa dziko la pansi, chifukwa cha malipenga omwe asalira kuti alizidwe na angelo atatu."

1
08/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 8

1
09/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 9 \v 1 \v 2 Ndipo mngelo wa cisanu analiza lipenga yake. Ninaona nyenyezi kumwamba yamene inagwa pa dziko la pansi. Nyenyezi inapasiwa makiyi yosegulira mugodi opanda kolekezera. Inasegula khomo la mugodi opanda kolekezera, ndipo panachoka utsi monga uchoka pa muliro waukulu. Dzuwa na mphepo zinadesedwa chifukwa cha utsi ochokera ku mugodi wamene uyu.

1
09/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 Kuchoka mu utsi dzombe unabwera pa dziko la pansi, ndipo inapasidwa mphamvu monga za kaliza pa dziko la pansi. Yanauziwa kuti yasaononge mitengo kapena udzu pa dziko, koma chabe anthu amene alibe chizindikiro cha Mulungu pa mphumi pao.

1
09/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 \v 6 Sibanapasidwe mphamvu zakupha anthu, koma kuwavutisa chabe kwa miyezi isanu. Ululu wake unali monga wa kaliza ngati waluma munthu. Masiku ameneo anthu azafuna imfa, koma osaipeza. Azafuna maningi kuti afe, koma imfa izathaba.

1
09/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 \v 8 \v 9 Dzombe inaoneka monga kavalo okonzekera nkhondo. Pa mitu zao panali makolona agolide, ndipo nkhope zao zinali monga za munthu. Anali na sisi monga mkazi, ndipo meno yanali monga ya nkhalamu. Yanali na vobisa pa chifuwa monga va nsimbi, ndipo chongo chao chinali monga cha akavalo ambiri opita ku nkhondo.

1
09/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 \v 11 \v 12 Yanali na michila yolumila monga ya kaliza; ku michila yanali na mphamvu yoluma anthu kwa miyezi isanu. Anali na wina monga mfumu pa iwo mngelo wa ku mugodi opanda kolekezera. Dzina lake mu chi heberi anali Abaddoni, ndipo mu chi greek anali na dzina lakuti Apollyon. Soka loyamba lapita. Onani! pambuyo pa izi pali zilango zina zomwe zibwera.

1
09/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 \v 14 \v 15 Mngelo wa namba 6 analiza lipenga lake, ndipo ninamva mau ochokera mu nyanga ya pa guwa la golide yomwe ipezeka kwa Mulungu. Liu linanena na mngelo wa nambala 6 yemwe anali na lipenga, "masula angelo anai omwe niomangiwa pa msinje waukulu wa Euphrates." Angelo anai omwe anakonzedwera nthawi imenei, siku limeneli, mwezi umeneo na chaka chimenechi, anamasulidwa kuti aphe gawo lina la anthu.

1
09/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 \v 17 Nambala ya anthu omwe anali pa msana wa akavalo ianali 200,000,000. Ninamva nambala yao. Umu ni mwamene ninaonera akavalo mu masomphenya yanga na iwo okwerapo. Zovala pa zifuwa zao zinali zofiilira, zooneka bulumu ni zachikasu. Mitu ya akavalo imaoneka monga mitu ya nkhalamu, ndipo mkamwa mwao mumatuluka moto, utsi, na sufule.

1
09/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 \v 19 Gawo lalikulu la anthu anafa chifukwa cha zilango zitatu zimenezi: Moto, utsi na sufule zomwe zinachoka mukamwa mwao. Pakuti mphamvu ya akavalo inali mkamwa mwao na ku muchila kwao- chifukwa michila yao inali ngati njoka, ndipo inali na mitu yamene inali kupwetekera anthu.

1
09/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 \v 21 Anthu ena onse, aja amene sanaphewe na zilango zimenezi, sanalape zoipa zamene anachita, kapena kuleka kupembeza ziwanda na mafano ya golide, siliva, bronze, minyala, na mitengo-zinthu zomwe sizipenya, kumva kapena kuyenda. Sanalapenso pa kupha kwao, matsenga yao, chiwelewele chao kapena ncito zao za kuba.

1
09/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 9

View File

@ -1 +1,5 @@
\c 11 \v 1 Nteete ina pasiwa kuli ine kuti ni isebenzese monga mutengo opimila. Ni nauziwa "Ima upime tempele ya Mulungu na luwa, na bamene ba pempelelamo. \v 2 Koma usapime lubanza panja pa tempele, chifukwa yapasiwa ku ochimwa. Bazadya-dyaka muzinda oyera kufikila myezi 42.
<<<<<<< HEAD
\c 11 \v 1 Nteete ina pasiwa kuli ine kuti ni isebenzese monga mutengo opimila. Ni nauziwa "Ima upime tempele ya Mulungu na luwa, na bamene ba pempelelamo. \v 2 Koma usapime lubanza panja pa tempele, chifukwa yapasiwa ku ochimwa. Bazadya-dyaka muzinda oyera kufikila myezi 42.
=======
\c 11 \v 1 \v 2 Tete inapasiwa kwa ine kuti nisebenzese monga chopimira. Ninauziwa ati, " Nyamuka upime kachisi ya Mulungu na guwa, na onse amene apembeza mwamene. Koma osapima panja pa kachisi, chifukwa papasiwa kwa amitundu. Azaponda mzinda oyera kwa miyezi 42.
>>>>>>> e420be4f253cdc4b36bad4180b49a52aeb350723

1
front/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Chibvumbuluso

View File

@ -36,11 +36,12 @@
"Alpen Banda",
"Jane Kuntashula",
"moses zulu",
"GEORGE NKHOMA"
"GEORGE NKHOMA",
"George Nkhoma",
"george nkhoma"
],
"finished_chunks": [
"11-title",
"11-01",
"11-03",
"11-06",
"11-08",