Tue Jan 22 2019 20:31:46 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-22 20:31:46 +02:00
parent ff167cc9a9
commit e7adc1db5b
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Ine, Yohane-m'bale wanu amene agabana na inu zobvuta na kupilira zamene zipezeka mwa Yesu- ninali pa malo ozungulilidwa na manzi ya Patmos kamba ka mau ya Mulungu na umboni wa Yesu. Ninali mu mzimu wa siku la ambuye. Ninamvera kumbuyo kwanga mau okuwa omveka monga lipenga. Yanakamba ati, "lemba zamene uona mu buku, elo uzitume ku mipingo isanu na iwiri- ku Efeso, ku Smyrna, ku Pergamum, ku Thyatira, ku Sardis,
\v 9 \v 10 \v 11 Ine, Yohane-m'bale wanu amene agabana na inu zobvuta na kupilira zamene zipezeka mwa Yesu- ninali pa malo ozungulilidwa na manzi ya Patmos kamba ka mau ya Mulungu na umboni wa Yesu. Ninali mu mzimu wa siku la ambuye. Ninamvera kumbuyo kwanga mau okuwa omveka monga lipenga. Yanakamba ati, "lemba zamene uona mu buku, elo uzitume ku mipingo isanu na iwiri- ku Efeso, ku Smyrna, ku Pergamum, ku Thyatira, ku Sardis, ku Philadelphia na ku Laodicea.