Thu Jan 24 2019 11:55:04 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-24 11:55:04 +02:00
parent 2904f3537e
commit 9b0b55f82e
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 Imozi mwa zamoyo zinai inapasa angelo 7 mbale za golide 7 za mkwiyo wa Mulungu,
\v 7 \v 8 Imozi mwa zamoyo zinai inapasa angelo 7 mbale za golide 7 za mkwiyo wa Mulungu, zamene zinkhala muyayaya. Tempile inazaziwa na utsi wa ukulu wa Mulungu na mphamvu zake. Palibe amene analobamo mpaka pamene zilango zonse 7 zinatha.