Thu Jan 24 2019 12:43:04 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-24 12:43:04 +02:00
parent c07b281058
commit 465c005fc5
2 changed files with 2 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 \v 11 Mngelo wa cisanu anathira mbale yake pa mpando wa chilombo, ndipo mdima unaphimba umfumu wake. Anakukuta malilime ao chifukwa cha kuwawa. Ananyoza zina la Mulungu chifukwa
\v 10 \v 11 Mngelo wa cisanu anathira mbale yake pa mpando wa chilombo, ndipo mdima unaphimba umfumu wake. Anakukuta malilime ao chifukwa cha kuwawa. Ananyoza zina la Mulungu chifukwa cha kuwawa na zilonda, koma anakana kulapa zoipa zomwe anali kuchita.

1
16/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 \v 13 \v 14 Mngelo wa nambala 6 anathira mbale yake mu m