Tue Jan 22 2019 19:57:46 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-22 19:57:46 +02:00
parent 0a454ff7a4
commit 31cd9a2cd1
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\c 1 \v 1 \v 2 \v 3 Ili ni vumbuluso la Yesu Kristu lamene Mulungu anamupasa kuti aonese akapolo ake zamene zizacitika manje-manje. Anazionesa kupitira mwa mngelo wake kwa Yohane. Yohane anacitira umboni mau a Mulungu
\c 1 \v 1 \v 2 \v 3 Ili ni vumbuluso la Yesu Kristu lamene Mulungu anamupasa kuti aonese akapolo ake zamene zizacitika manje-manje. Anazionesa kupitira mwa mngelo wake kwa Yohane. Yohane anacitira umboni mau a Mulungu na pa umboni operekedwa wa Yesu Khristu, zinthu zonse zamene anaona.