Tue Nov 05 2019 10:11:13 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-11-05 10:11:14 +02:00
parent 90ae23fb55
commit 3110ae2336
2 changed files with 2 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
yerusalemu anali na ulemelero wa mulungu, na kuwala kwake kunali monga mphete, monga mwala wa bafuta wa jesipa. unali na mpanda waukulu, na polowera 12, na angelo pa khomo. pa makomo onse panalembewa maina ya mitundu 12 ya ana a israele. ku m'mawa kunali makomo atatu, kumpoto
\v 11 \v 12 \v 13 yerusalemu anali na ulemelero wa mulungu, na kuwala kwake kunali monga mphete, monga mwala wa bafuta wa jesipa. unali na mpanda waukulu, na polowera 12, na angelo pa khomo. pa makomo onse panalembewa maina ya mitundu 12 ya ana a israele. ku m'mawa kunali makomo atatu, kumpoto kunali makomo atatu, ku m'mwera kunali makomo atatu komanspo kumazulo kunali makomo atatu.

1
21/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
mpanda wa mzinda unali ni maziko 12, pa izo panali maina 12 ya apositoli a mwana wa nkhosa. wamene anakamba na ine anali na kopimila kopangiwa na golide kamene