Thu Jan 24 2019 12:55:04 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-01-24 12:55:05 +02:00
parent 2d274c9137
commit 27156f5025
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 12 \v 13 \v 14 Mngelo wa nambala 6 anathira mbale yake mu msinje waukulu wa Euphrates. Manzi yake yanauma kupanga njira ya mamfumu yamene yanachokera ku m'mawa. Ninaona mizimu yoipa yomwe yanaoneka monga achule kutuluka mkamwa mwa chinjoka, mwa chilombo na mwa mneneri wa boza. Chifukwa ni mizimu ya ziwanda kuchita milakuli ni zizindikiro. Anali kupita kwa mamfumu a ziko lonse kuwaso
\v 12 \v 13 \v 14 Mngelo wa nambala 6 anathira mbale yake mu msinje waukulu wa Euphrates. Manzi yake yanauma kupanga njira ya mamfumu yamene yanachokera ku m'mawa. Ninaona mizimu yoipa yomwe yanaoneka monga achule kutuluka mkamwa mwa chinjoka, mwa chilombo na mwa mneneri wa boza. Chifukwa ni mizimu ya ziwanda kuchita milakuli ni zizindikiro. Anali kupita kwa mamfumu a ziko lonse kuwasonkhanisa pamozi kukonzekera nkhondo pa siku lalikulu la ambuye amphamvu zonse.