diff --git a/15/02.txt b/15/02.txt new file mode 100644 index 0000000..6cd7165 --- /dev/null +++ b/15/02.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 2 Ninaona chamene chinaoneka monga nyanja ya galasi yosakaniza na muliro. Amene anaimilira pa mbali ya nyanja ni aja amene anapambana chilombo na fano lake, na nambala yamene iimilira zina lake. \ No newline at end of file