diff --git a/07/15.txt b/07/15.txt index 1197641..2c0d6e6 100644 --- a/07/15.txt +++ b/07/15.txt @@ -1 +1 @@ -\v 15 \v 16 \v 17 Pa chifukwa ichi, ali pa maso pa mpando wa Mulungu, ndipo amiupembeza usana na usiku mu nyumba yake. Iye wamene ankhalaa pa mpando wa chimfumu azaika tenti yake pa iwo. Sazamveranso njala, kapena kumvera ludzu. Dzuwa sizawagwesa, kapena kutenthewa. Chifukwa mwana wa nkhosa pakati pa mpando azankhala mbusa wao, ndipo azawapereka ku malo a manzi ya moyo, \ No newline at end of file +\v 15 \v 16 \v 17 Pa chifukwa ichi, ali pa maso pa mpando wa Mulungu, ndipo amiupembeza usana na usiku mu nyumba yake. Iye wamene ankhalaa pa mpando wa chimfumu azaika tenti yake pa iwo. Sazamveranso njala, kapena kumvera ludzu. Dzuwa sizawagwesa, kapena kutenthewa. Chifukwa mwana wa nkhosa pakati pa mpando azankhala mbusa wao, ndipo azawapereka ku malo a manzi ya moyo, ndipo Mulungu azapukuta misozi mu menso yao." \ No newline at end of file diff --git a/08/01.txt b/08/01.txt new file mode 100644 index 0000000..8064ff2 --- /dev/null +++ b/08/01.txt @@ -0,0 +1 @@ +\c 8 \v 1 \v 2 Pamene mwana wa nkhosa anasegula chizindikiro cha namba 7, kunali \ No newline at end of file diff --git a/08/title.txt b/08/title.txt new file mode 100644 index 0000000..827e81c --- /dev/null +++ b/08/title.txt @@ -0,0 +1 @@ +Mutu 8 \ No newline at end of file