nya-x-nyanja_rev_text_reg/07/11.txt

1 line
330 B
Plaintext
Raw Permalink Normal View History

\v 11 Angelo onse anali oimilira kuzungulira mpando wa chimfumu na kuzungulira akulu komanso zamoyo zinai, ndipo anagwa pansi kuyang'ana nkhope zao pansi kulambira pa mpando wa chimfumu. Anapembeza Mulungu, \v 12 kukamba kuti, "Amen! matamando, ulemelero, nzeru, mayamiko, ulemu, mphamvu, zinkhale kwa Mulungu nthawi zonse! Amen!"