\v 15 Zoonadi ndikuuzani inu, aliyense amene sazalandila ufumu wa Mulungu ngati kamwana kang'ono sazalowa."
\v 16 Ndipo anathenga ana m'manja ake ndikutudalisa pamene anatusanjika manja ake pa tiana.