1 line
388 B
Plaintext
1 line
388 B
Plaintext
\v 46 Ndipo anapyamo ku Yeliko. pamene anacoka ku Yeliko ndi wophunzira ake, ndi anthu ambiri, mwana wa Timaulesi, Batulumewo, mpofu yopempha, inakhala panjira. \v 47 Pamene anamva kuti niYesu waku Nazalete, anayambakukuwa nati, "Yesu , mwana wa Davide, nicitire cifundo!" \v 48 Ambiri anazuzula mpofu ija, muuzeni kuti akhale cete. koma analirisa, "Mwana wa Davide, nicitilecifundo ine!" |