nya-x-nyanja_mrk_text_reg/06/39.txt

1 line
348 B
Plaintext

\v 39 Anawalamulila kuti ankhale mphasi mumagulupu pa uzu wa msipu. \v 40 Ndipo anankhala mumagulupu; magulupu ya mahundredi (100) ndi mafifte (50). \v 41 Anathenga mitanda isanu ya buledi ndi nsomba ziwili, ndipo anayangana kumwamba ndikuyidalitsa ndi kusuna ndikupasa wophunzila ake kuti apase anthu. Ndipo anagawana nsomba zija ziwili kwa wonse.