1 line
345 B
Plaintext
1 line
345 B
Plaintext
\v 30 Panthawi yamene ijaYesu anazindikila kuti mpamvu zacoka muli iye. Ndipo anayangana kumbuyo kwamene kunali anthu ambiri nafunsa nati, "Ndani wanikuza covala canga?" \v 31 Wophunzila ake anati, "Muona anthu awa ambiri alikukugundani, ndipo inu mulikunena kuti, 'ndani wakugwilani?"' \v 32 Koma Yesu anayangana kuti amuone wamene anacita izi. |