nya-x-nyanja_mrk_text_reg/05/28.txt

1 line
185 B
Plaintext

\v 28 Cifukwa anati, "Ngati ndingagwileko cabe covala cake, ndizacilisika." \v 29 Pamene anamugwila iye, magazi analeka kucoka, ndipo anamvela mutupi mwake kuti acilisika kumatenda aja.