nya-x-nyanja_jos_text_reg/14/06.txt

1 line
376 B
Plaintext

\v 6 Pamenepo mutundu wa Ayuda vnabwela kuli Yoswa pa Giligala. Calebu mwana Jephunneh mu kenizzite, anakamba kuli yeve,'' uziba zamene Yehova anakamba kuli Mose munthu wa mulungu pali iwe na ine pa kadesh Barnea. \v 7 Ninali nazaka fote pamene Mose mtumiki wa Yehova ananituma kucoka ku kadesh Barnea ukabona malo. Ni Nbwesa mau kuli yeve monga cinali mumitima mwanga kupanga