nya-x-nyanja_jos_text_reg/09/09.txt

1 line
269 B
Plaintext
Raw Normal View History

banakamba kuli iye,'' Batumitiki bako babwela kuno kucokela kumalo yakutali, cifukwa ca zina ya Yehova mulungu wanu. Tamvela pali yeve na pali vonse anacita mu Eigipito - navonse anacita kuli mafumu yabili yako Amoni kumbali ina ya Yolodani - kuli sihon mfumu ya Heshbo