nya-x-nyanja_job_text_reg/33/25.txt

1 line
256 B
Plaintext

\v 25 Pamenepo mnofu wake ukhala wosalala kuposa mwana; wabwezeretsedwa m'masiku a ubwana wake. \v 26 Adzapemphera kwa Mulungu, ndipo Mulungu adzamukomera mtima, kotero kuti adzawona nkhope ya Mulungu ndi chimwemwe. Mulungu apatsa munthu chigonjetso chake.