\v 20 Pakati pa kuseni na mumazulu bama onongeka; bana onongeka muyayaya kulibe aliense wakubzindikila. \v 21 Kodi zingwe za mahema yao sizidulidwa pakati pawo? Bamafa; bamafa ninshi kulibe nzelu.