nya-x-nyanja_job_text_reg/34/31.txt

1 line
348 B
Plaintext

\v 31 Munthu wina akauza Mulungu kuti, 'Ine ndachimwa, koma sindichimwanso; \v 32 ndiphunzitseni zomwe sindingathe kuziona; Ndachita tchimo, koma sindidzachitanso. ' \v 33 Kodi mukuganiza kuti Mulungu adzalanga tchimo la munthu ameneyo, popeza simukukonda zomwe Mulungu amachita? Muyenera kusankha, osati ine. Chifukwa chake nenani zomwe mukudziwa.