nya-x-nyanja_job_text_reg/34/21.txt

1 line
283 B
Plaintext

\v 21 Pakuti maso a Mulungu amayang'ana njira za munthu; amapenya mayendedwe ake onse. \v 22 Palibe mdima, kapena mdima wandiweyani kumene ochita zosalungama angabisalire. \v 23 Pakuti Mulungu safunikiranso kusanthula munthu; palibe chifukwa choti munthu aliyense apite kukamuweruza.