nya-x-nyanja_job_text_reg/34/16.txt

1 line
176 B
Plaintext

\v 16 Ngati tsopano muli ndi chidziwitso, mverani ichi; mverani mawu anga. \v 17 Kodi amene amadana ndi chilungamo angalamulire? Kodi muweruza Mulungu, wolungama ndi wamphamvu?