nya-x-nyanja_job_text_reg/34/13.txt

1 line
278 B
Plaintext

\v 13 Ndani anamuika woyang'anira dziko lapansi? Ndani adaika dziko lonse pansi pake? \v 14 Ngati angakhazikitse zolinga zake pa iye yekha, ndipo ngati angabwezeretse kwa iye mzimu wake ndi mpweya wake, \v 15 pamenepo anthu onse adzawonongeka pamodzi; anthu adzabwerera kufumbi.