nya-x-nyanja_job_text_reg/34/07.txt

1 line
267 B
Plaintext

\v 7 Ndi munthu uti amene angafanane ndi Yobu, amene amamwa zopanda pake ngati madzi, \v 8 amene amayenda m thegulu la anthu ochita zoyipa, ndipo amayenda ndi anthu oyipa? \v 9 Pakuti iye anati, 'Sizothandiza kwa munthu kusangalala ndi zinthu zimene Mulungu amafuna.'