nya-x-nyanja_job_text_reg/34/04.txt

1 line
289 B
Plaintext

\v 4 Tiyeni tisankhe tokha chomwe chiri cholungama: tizindikire pakati pathu chomwe chili chabwino. \v 5 Pakuti Yobu anati, 'Ine ndine wolungama, koma Mulungu wandilanda. \v 6 Kaya ndili ndi ufulu wotani, ndimaonedwa kuti ndine wabodza. Chilonda changa sichitha, ngakhale ndilibe uchimo. '