nya-x-nyanja_job_text_reg/34/01.txt

1 line
172 B
Plaintext

\c 34 \v 1 Elihu anapitiriza kulankhula kuti: \v 2 “Tamverani mawu anga, anzeru inu, ndimvereni, inu akudziwa. \v 3 Pakuti khutu liyesa mawu, monga m'kamwa mulawa kulawa.