nya-x-nyanja_job_text_reg/22/12.txt

1 line
254 B
Plaintext

\v 12 Si Mulungu ankala kutali maningi kumwamba? yangana kutalimpa kwa nyenyezi, patali pamene zilili! \v 13 Mukuti, 'Mulungu aziba cani? angaweluze mu mudima ukulu? \v 14 Makumbi yotikama yamuvinikila, mwakuti samationa; amayenda pa cikumbi cakumwamba.'