nya-x-nyanja_job_text_reg/11/04.txt

1 line
332 B
Plaintext

\v 4 Iwe umati kwa Mulungu, 'Zikhulupiriro zanga ndi zoyera, ndipo ndimakhala wopanda cholakwa pamaso panu.' \v 5 Koma, o, Mulungu akanati alankhule ndi kukutsegulirani milomo yake; \v 6 kuti akakuwonetse zinsinsi za nzeru! Pakuti iye ndi wozindikira kwambiri. Dziwani tsono kuti Mulungu amafuna kwa inu zochepa zopyola muyeso wanu.